Misa ya Devine Mercy Apostolate mu Arkidayosizi ya Lilongwe (Kachebere Parish) Titelbild

Misa ya Devine Mercy Apostolate mu Arkidayosizi ya Lilongwe (Kachebere Parish)

Misa ya Devine Mercy Apostolate mu Arkidayosizi ya Lilongwe (Kachebere Parish)

Jetzt kostenlos hören, ohne Abo

Details anzeigen

Über diesen Titel

Pa 12 April 2025, bungwe la Devine Mercy Apostolate mu arkidayosizi ya Lilongwe, linachita mwambo wamapemphero ku malo woyera a Kachebere m'boma la Mchinji, ngati mbali imodzi yokonzekera chaka cha pasaka.

Pa mwambowu ansembe anapereka Sacramento lakulapa kwa akhristu omwe anafika pamalowa.

Monsignor Patrick Thawale anapereka chiphunzitso kwa atumiki abungweli pa mutu wakuti "kukhala a paulendo a chiyembekezo," maaka pomwe mpingo waKatolika uli mkati mwa chaka cha Jubilee ya chiyembekezo.

Zitatha zonse, Monsignor Thawale anatsogolera mwambo wansembe ya Misa ndipo utatha mwambowu, akhristu anakachita mapemphero anjira ya mtanda yokwera phili la Kalulu.

Das sagen andere Hörer zu Misa ya Devine Mercy Apostolate mu Arkidayosizi ya Lilongwe (Kachebere Parish)

Nur Nutzer, die den Titel gehört haben, können Rezensionen abgeben.

Rezensionen - mit Klick auf einen der beiden Reiter können Sie die Quelle der Rezensionen bestimmen.